nya-x-nyanja_jer_text_reg/30/06.txt

1 line
351 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 6 \v 7 Funsani ndikuwona ngati mwamuna abereka mwana. Nchifukwa chiyani ndimaona mnyamata aliyense ali ndi dzanja mchiuno mwake ngati mkazi wobereka mwana? Nchifukwa chiyani nkhope zawo zonse zatuwa? Tsoka! Pakuti tsikulo lidzakhala lalikulu, lopanda lofanana nalo. Idzakhala nthawi ya nkhawa kwa Yakobo, koma adzapulumutsidwa ku nthawiyo.