kdn_rom_text_reg/15/30.txt

1 line
466 B
Plaintext

\v 30 Ndinifuna kukulimbisani abale wangu, kuchokela mwaMpfumu Yesu Kristu nachikondi chatinipasiwa naMzimu, phatanani nainepo mumapemphelo. \v 31 Pemphelani kuti Mulungu andibhasepe bwino mumanja mwaawo asingakhulupilile wamuJudeya. pemphelani pomwe kuti wanthu waMulungu ali muJelusalemu akondwe pakuwathandiza kwandizayita. \v 32 Pemphelani kuti ndizabwelele nakukwanu ndichikondwa kana nakufuna kwaMulungu, ndiye ndinizakondwa nakupuma thangwe lakukuzungilani.