nya-x-nyanja_1pe_text_reg/03/18.txt

1 line
367 B
Plaintext

\v 18 \v 19 \v 20 klistu neye anavutika chifukwa chamachimo yatu.eve oyela anatifela,enze oyela,kuti atibwelese kwa mulungu.anpaiwa kumubili koma anauka kumuzimu.mwamuzimu,anapita kulalikila kuba mundende.sibana nvelele pamene mulungu anba yembekezela mumadaizi yanowa.mumadaizi yopanga chiboti namulungu anapulumusa bantu bangono-moyo zili chabe eety.kupita mumanzi.