\v 3 Asachite na zoonekela kunja: nazibango zovala kumanja za golidena zovala. \v 4 Mumalo mwake lekani zichitike na mtima wonse, nakukongola kwa bwino kwa mu mzimu, yokongola kwa mulungu.