nya-x-nyanja_1pe_text_reg/04/17.txt

1 line
356 B
Plaintext

\v 17 Chifukwa ntawi ya chiweluzo chiyamba na nyumba ya Mulungu, chikayamba naise, nanga kuli baja ba mene siba nvelela mau ya Mulungu? \v 18 Kapena muntu oyela azavutikila kungena kumwamba nanga chizankhala bwanji kuli muntu amene saziba Mulungu? \v 19 Lekani bamene bavutika kamba ka Mulungu baike umoyo wao kuo kulupilika anapanga vonse bwino.