\v 15 Monga anakuitanani nioyela,nkalani oyela,nkalani oyela muzonse zochita zanu \v 16 .Pakuti nicholembewa;nkalani oyela,chifukwa ndine oyela \v 17 .Ndiye pamene muitana kuti atate amene amaweluza osapita kumbali koma kulingana nanchito yamene aliyense agwila,tayani ntawi yaulendo wanu naulemu.