1 line
325 B
Plaintext
1 line
325 B
Plaintext
\c 20 \v 1 \v 2 \v 3 ninaona mungelo wamene anachoka ku mwamba. anali na makiyi ya kumugodi opanda kolekezera, elo anali na tcheni ikulu maningi mumanja mwake. anagwira chinjoka, chamene ni mudyerekezi, kapena satana, na kumumanga kwa zaka 1000. anamuponya mu chimugodi, elo anavalapo. banachita izi kuti asanamize futi maiko |