nya-x-nyanja_rev_text_reg/22/16.txt

1 line
150 B
Plaintext

\v 16 ine, yesu, natuma mungelo wanga kuti acite umboni kwa inu pa zinthu izi kwa mipingo. ndine muzu wa mbadwo wa davide, nyenyezi ya m'mawa yowala."