nya-x-nyanja_rev_text_reg/21/01.txt

1 line
277 B
Plaintext

\c 21 \v 1 \v 2 elo ninaona kumwamba kwasopano na ziko lapansi lasopano, cifukwa kumwamba na ziko ya kudala vinapita, na nyanja sizinaliko. ninaona muzinda oyera, yerusalemu wa sopano, zamene zinachoka kumwamba kwa mulungu, kukonzewa monga mkazi wamene akumana na mwamuna wake.