nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/01.txt

1 line
306 B
Plaintext

\c 14 \v 1 \v 2 Ninaona na kuona mwana wa nkhosa oimilira pa phiri la Zion. Anali na anthu 144,000 amene anali na zina lake na zina la Atate ake yolembewa pa mphumi zao. Ninamvera mau ochokera kumwamba omveka monga manzi yambiri na kugunda kwa mphamvu. Mau omwe ninamvera yanali monga anthu oliza mitoliro.