nya-x-nyanja_rev_text_reg/09/01.txt

1 line
356 B
Plaintext

\c 9 \v 1 \v 2 Ndipo mngelo wa cisanu analiza lipenga yake. Ninaona nyenyezi kumwamba yamene inagwa pa dziko la pansi. Nyenyezi inapasiwa makiyi yosegulira mugodi opanda kolekezera. Inasegula khomo la mugodi opanda kolekezera, ndipo panachoka utsi monga uchoka pa muliro waukulu. Dzuwa na mphepo zinadesedwa chifukwa cha utsi ochokera ku mugodi wamene uyu.