nya-x-nyanja_rev_text_reg/04/09.txt

1 line
507 B
Plaintext

\v 9 \v 10 \v 11 Nthawi zonse pamene za moyo zipereka ulemelero, ulemu na matamando kwa amene ankhala pa mpando wa chimfumu, wamene ankhala kwa muyaya, akulu 24 amazigwesa pansi kulambira iye amene ankhala pa mpando wa chimfumu. Bamagwada kwa iye amene ankhala muyaya, ndipo amaponya pansi ma kolona yao ku mpando, kukamba kuti, "Ndinu oyenera, ambuye athu na Mulungu wathu, kulandira ulemu, ulemelero ndi mphamvu. Chifukwa munalenga zinthu zonse, ndipo mwa chifuniro chanu, zinankhalako ndipo zinalengewa."