1 line
320 B
Plaintext
1 line
320 B
Plaintext
\v 3 \v 4 Kumbukirani, sopano, zamene munalandira na kumvera. Gonjerani, na kulapa. Koma ngati simuzauka, nizabwera monga kawalala, elo simuzaziba nthawi yamene nizabwelera kwa inu. Koma pali maina yang'ono chabe ya banthu mu Sardis bamene sibanafipise vovala vao. Bazayenda naine, mu zobvala zoyera, chifukwa nioyenera. |