nya-x-nyanja_rev_text_reg/09/20.txt

1 line
319 B
Plaintext

\v 20 \v 21 Anthu ena onse, aja amene sanaphewe na zilango zimenezi, sanalape zoipa zamene anachita, kapena kuleka kupembeza ziwanda na mafano ya golide, siliva, bronze, minyala, na mitengo-zinthu zomwe sizipenya, kumva kapena kuyenda. Sanalapenso pa kupha kwao, matsenga yao, chiwelewele chao kapena ncito zao za kuba.