nya-x-nyanja_rev_text_reg/17/06.txt

1 line
324 B
Plaintext

\v 6 Ninaona kuti mkazi anali wokolewa na magazi ya bakukhulupilila na magazi ya opaiwa pa cifukwa ca Yesu. Pamene nina muona, nina dabwisiwa kwambili. \v 7 Koma mngelo ananena kuli ine, "wadabwila ciani? nizakufotokozerani tanthauzo ya mkazi na cinyama cimene cinali ku munyamula, cilombo cimene cili na mitu 7 na nyanga 10