\v 11 Nina ona chilombo china chichokela pa ziko yapansi. Chinali na nsengo zibili monga ka mwana ka nkhosa, chinali kukamba monga chilombo.