nyanja zinachosa bamene banaferamo. imfa na hadesi zinachosa bakufa bamene banalimo, elo bakufa banaweruziwa kulingana na zamene banachita. imfa na hadesi zinaponyewa mu nyanja ya muliro. uku nikufa kwa chiwiri- nyanja ya muliro. ngati zina ya wina aliyense sinalembewe mu buku la moyo, anaponyewa mu nyanja ya muliro.