\c 18 izi zitasila ninaona futi mungelo winangu aseluka kuchoka ku mwamba. anali na mpamvu zambiri, elo ziko inawala kamba ka ulemelero wake. 2 anapunda na mau yakulu, kukamba ati, ̈ agwa, agwa babylon wa mpamvu! wankhala malo yonkhalako ziwanda, konkhala mizimu yoipa na kobisala mizimu yonyansana nyoni zosaloledwa. 3 kabili maiko yonse yamwa vinyo wa chigololo. mamfumu ya muziko