\v 6 \v 7 mungelo anakamba kwa ine, "mau aya ni yokulupilika komanso ya zoona. ambuye, mulungu wa mizimu ya aneneli, anatuma mungelo wake kuonesa akapolo ake zamene zizacitika posacedwa." "ona! nibwera manje-manje! odala bamene bamvera mau yanga ya uneneri ya mu buku iyi."