\v 14 mpanda wa mzinda unali ni maziko 12, pa izo panali maina 12 ya apositoli a mwana wa nkhosa. \v 15 wamene anakamba na ine anali na kopimila kopangiwa na golide kamene anapimila mzinda, makomo na mpanda wake.