\v 7 Imozi mwa zamoyo zinai inapasa angelo 7 mbale za golide 7 za mkwiyo wa Mulungu, zamene zinkhala muyayaya. \v 8 Tempile inazaziwa na utsi wa ukulu wa Mulungu na mphamvu zake. Palibe amene analobamo mpaka pamene zilango zonse 7 zinatha.