Thu Jan 24 2019 17:15:01 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
commit
f7092dbab4
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 10 \v 1 Pamene apo ninaona m'ngelo wina wamphamvu aseluka kucokela ku mwamba. Anavimbiwa na mukumbi, panali futi na uta wa leza pa mwamba pa mutu wake. Cinso cake cinali ngati zuba na mapazi yake yenze monga vipilala va mulilo. \v 2 Anali naka buku kakang'ono mu manja yake yamene yinali yosegula, na kuika kwendo la ku kwanja la manja pa cimumana na yakumanzele pa mtunda.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 3 Pamene apo anapunda namau yopundisa monga ku uluma kwa mkango. Pamene anapunda, zo gunda 7 vinakamba nakuuluma kwake. \v 4 Pamene vogunda 7 vinakamba, nenze pafupi na kulemba, koma ninamvela mau kucokela ku mwamba yakunena, "Sunga nkama ya vimene vogunda 7 vanena. Usavilembe."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 5 pamene apo mngelo amene nenze naona kuimilila pa mmana na pa calo, ananyamula kwanja lake lamanja ku mwamba. \v 6 Analumbila pa yeve ankala na moyo nthawi yonse, amene anapanga mumwamba na vonse vili mwa mene umo, calo na vonse vili mwa mene, na cimumana na vonse vili mwamene, na mngelo anakamba, "Sikuzankhala futi kucedwa. \v 7 Koma pa siku yamene mngelo wa 7 ali pafupi na kuliza mtolilo, pamene apo codadwisa ca Mulungu cizakwanilisika, monga mwamene ananena ku ba nchito bake maporofita."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 8 Mau ninamvera kucokela ku mwamba yanalankhulanso kuli ine: "Pita, tenga buku losegula imene ili mu kwanja ya mngelo woimilila pa mumana na pa ziko." \v 9 Pamene apo ninayenda ku mungelo nakumuuza kuti anipase ka buku kakang'ono. Anakamba na ine, "Tenga buku na kudya. Izapanga mmala mwako ku baba, koma mkamwa mwako izankala yonzuna ngati uci."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 10 Nina tenga kabuku kakang'ono kucoka ku manja a mngelo na kudya. Inali yonzuna monga uci mukamwa mwanga, nitasiliza kudya, mumala mwanga munababa. \v 11 Pamene apo wina anakamba na ine, ukambenso za anthu ambili, mitundu, malilime na mamfumu."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 10
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 17 \v 1 Mmozi wa angelo 7 anali anyamula mbale 7 anafika nakunena kuli ine, "Bwela, nizakuonesa cizuzulo ca hule ya mahule wonkhala pa mipando ya mbili pa mmana. v \v 2 Ni pamulandu wa yeve ma mfumu ya pa calo acita macimo ya cigololo. Na onkhala pa ziko banakolewa na moba wa cimo yake yacigololo."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 3 Pamene apo mungelo ananinyamula mu mzimu kupita kusanga, kumene ninaona mkazi bonkhala pa cinyama cosweta cenze cozula namazina yamaboza. Ici cinyama cenze na mitu 7 na masengo 10. \v 4 mzimai enze anavala za pepo na zosweta banamuvalika za golide, myala yo dula, namaulungu. Enze anagwila mumanja kapu ya golide yozula na vinthu voipa na vadothi va ucimo wa cigololo cake. \v 5 Pamphumi pake panalembewa zina la tanthauzo lobisika: "Babulo wa mkulu, mai wa avigololo na vinthu voipa va pa ziko."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 6 Ninaona kuti mkazi anali wokolewa na magazi ya bokhulupilila na magazi ya bopaiwa pa cifukwa ca Yesu. Pamene nina muona, nina dabwisiwa kwambili. \v 7 Koma mngelo ananena kuli ine, "wadabwila ciani? nizakufotokozerani tanthauzo ya mkazi na cinyama camene cimunyamula, cilombo camene cili na mitu 7 na nyanga 10
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 8 Cinyama munaona cinaliko, siciliko manje, koma cili pafupi kubwela kucokela mu cimgodi coyendelela. Pamene apo cizayenda kuononga. Awo bonkhala pa calo, bamene mazina ni yosalembewa mu buku ya bamoyo kucokela pamene ziko linapangiwa - bazadabwa pamene bazaona cinyama cinaliko, manje siciliko, koma cili pafupi na kubwela.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 9 Ici cifuna maganizo anzelu. Mitu 7 ni malupili 7 pamene mkazi ali nkhezi. \v 10 Pali na mafumu 7. mafumu 5 bagwa, m'mozi wasala, na wina akalibe kubwela; akabwela azankhalako pa ka nthawi kang'ono.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 11 cinyama camene cinaliko, koma manje siciliko, naceve nimfumu ya 8; koma ni cimozi ca mamfumu 7, naceve ciyenda mu kuonongeka.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 12 Nsengo 10 zimene munali mwaona ni mamfumu 10 amene akalibe kulandila malo akulamulila, koma bazalandila ulamulilo monga mafumu kwa ola imozi pamozi na cinyama. \v 13 Aba bali na ganizo imozi. kupeleka mphamvu na ulamulilo ku cinyama. \v 14 Bazacita nkhondo na Nkosa. Koma Nkosa izapambana cifukwa ni Mbuye wa ambuye na Mfumu ya mafumu - na pamozi naye pali woitiwa, wosankhiwa, na okhulupililika."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 15 Mngelo ananena kuli ine, "Manzi yamene unaona, pamene hule ya nkhala, banthu, magulu, mitundu, na malilime.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 16 Nyanga 10 zamene unawaona - beve na cinyama cizazonda hule. bazamupanga alibe kanthu na wacinthaku, bazadya nyama yake, ndipo bazamushokelatu na mulilo. \v 17 Pakuti Mulungu anaciika mumitima yao kucita colinga pa kuvomela kupeleka mphamvu ya kulamulila ku cinyama mpaka mau a Mulungu yakwanilisiwa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 18 Mkazi amene wenze waona ni tauni ya ikulu yamene ilamulila pa mafumu apa calo."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 17
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 18 \v 1 \v 2 \v 3 Vasila ivi vinthu ninaona mngelo wina kubwela pansi kucokela ku mwamba. Anali na ulamulilo ukulu, na ziko linaunikiliwa na ulemelelo wake. Anakuwa na mau amphamvu, na kunena, wagwa, wagwa ni babulo mkulu
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 18
|
|
@ -34,7 +34,8 @@
|
|||
"parent_draft": {},
|
||||
"translators": [
|
||||
"Alpen Banda",
|
||||
"Jane Kuntashula"
|
||||
"Jane Kuntashula",
|
||||
"moses zulu"
|
||||
],
|
||||
"finished_chunks": [
|
||||
"11-title",
|
||||
|
@ -47,6 +48,22 @@
|
|||
"11-15",
|
||||
"11-16",
|
||||
"11-18",
|
||||
"11-19"
|
||||
"11-19",
|
||||
"10-01",
|
||||
"10-03",
|
||||
"10-05",
|
||||
"10-08",
|
||||
"10-10",
|
||||
"17-title",
|
||||
"17-01",
|
||||
"17-03",
|
||||
"17-06",
|
||||
"17-08",
|
||||
"17-09",
|
||||
"17-11",
|
||||
"17-12",
|
||||
"17-15",
|
||||
"17-16",
|
||||
"17-18"
|
||||
]
|
||||
}
|
Loading…
Reference in New Issue