Wed Jan 23 2019 11:32:50 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
007927132b
commit
bef4f59e27
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 3 \v 4 \v 5 Palibe aliyense kumwamba, padziko la pansi kapena pansi pa dziko yemwe anali oyenera kusegula buku kapena kuwerenga. Ninalira maningi chifukwa panalibe aliyense oyenera kusegula kapena kuwerenga buku. Koma m'mozi wa akulu-akulu anati kwa ine, "Usalire. Ona! nkhalamu ya mtundu wa ayuda, muzu wa Davide, wapambana. Akwanisa kusegula buku na kusegula
|
||||
\v 3 \v 4 \v 5 Palibe aliyense kumwamba, padziko la pansi kapena pansi pa dziko yemwe anali oyenera kusegula buku kapena kuwerenga. Ninalira maningi chifukwa panalibe aliyense oyenera kusegula kapena kuwerenga buku. Koma m'mozi wa akulu-akulu anati kwa ine, "Usalire. Ona! nkhalamu ya mtundu wa ayuda, muzu wa Davide, wapambana. Akwanisa kusegula buku na kusegula zosindikizira zake."
|
Loading…
Reference in New Issue