Thu Jan 24 2019 09:36:15 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
0af258114a
commit
bea5fa9a5a
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 18 \v 19 Gawo lalikulu la anthu anafa chifukwa cha zilango zitatu zimenezi: Moto, utsi na sufule zomwe zinachoka mukamwa mwao
|
||||
\v 18 \v 19 Gawo lalikulu la anthu anafa chifukwa cha zilango zitatu zimenezi: Moto, utsi na sufule zomwe zinachoka mukamwa mwao. Pakuti mphamvu ya akavalo inali mkamwa mwao na ku muchila kwao- chifukwa michila yao inali ngati njoka, ndipo inali na mitu yamene inali kupwetekera anthu.
|
Loading…
Reference in New Issue