diff --git a/06/03.txt b/06/03.txt index 6d4a0a7..de6b6a9 100644 --- a/06/03.txt +++ b/06/03.txt @@ -1 +1 @@ -\v 3 \v 4 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha chiwiri, ninamvera chamoyo chachiwiri kukamba ati, "bwera!" Ndipo kavalo anatuluka osweta. Wamene anakwerapo anapasidwa mphamvu yochosa mtendere pa dziko la pansi, \ No newline at end of file +\v 3 \v 4 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha chiwiri, ninamvera chamoyo chachiwiri kukamba ati, "bwera!" Ndipo kavalo anatuluka osweta. Wamene anakwerapo anapasidwa mphamvu yochosa mtendere pa dziko la pansi, kuti anthu aphane okha-okha. Okwerapo ameneyu anapasidwa chimpeni chachikulu. \ No newline at end of file