Wed Jan 23 2019 10:26:50 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-23 10:26:50 +02:00
parent 2ea470af32
commit 884d90958a
2 changed files with 2 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 17 \v 18 Mukamba kuti, ndinu olemera, nili na zinthu zambiri, ndipo sinifuna kalikonse. Koma simuziba kuti ndinu ochitisa chifundo maningi, osauka, osapenya ni osabvala. Mvelani zamene nikamba: Gulani kwa ine golide oikidwa mu moto kuti munkhale olemera na zobvala zoyera zowala kuti mubvale musaonese manyazi ya umaliseche wanu, na \v 17 \v 18 Mukamba kuti, ndinu olemera, nili na zinthu zambiri, ndipo sinifuna kalikonse. Koma simuziba kuti ndinu ochitisa chifundo maningi, osauka, osapenya ni osabvala. Mvelani zamene nikamba: Gulani kwa ine golide oikidwa mu moto kuti munkhale olemera na zobvala zoyera zowala kuti mubvale musaonese manyazi ya umaliseche wanu, na mankhwala ya m'maso kuti uone bwino.

1
03/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 \v 20 Nimaphunzisa aliyense wamene