Thu Jan 24 2019 11:23:37 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
1f4f249dc1
commit
4522d239ec
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\c 10 \v 1 Pamene apo ninaona mngelo wamphamvu aseluka kucokela ku mwamba. Anavimbiwa na mukumbi, panali futi na uta wa leza pa mwamba pa mutu wake. Cinso cake cinali ngati zuba na mapazi yake yenze monga vipilala va mulilo. \v 2 Anali naka buku kakang'ono mu manja yake yamene yinali yosegula, na kuika kwendo lu ku kwanja la manja pa cimumana na yakumanzele pa mtunda.
|
||||
\c 10 \v 1 Pamene apo ninaona m'ngelo wina wamphamvu aseluka kucokela ku mwamba. Anavimbiwa na mukumbi, panali futi na uta wa leza pa mwamba pa mutu wake. Cinso cake cinali ngati zuba na mapazi yake yenze monga vipilala va mulilo. \v 2 Anali naka buku kakang'ono mu manja yake yamene yinali yosegula, na kuika kwendo lu ku kwanja la manja pa cimumana na yakumanzele pa mtunda.
|
Loading…
Reference in New Issue