Thu Jan 24 2019 10:35:04 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-24 10:35:04 +02:00
parent 3ffcb83127
commit 27db8333e4
2 changed files with 2 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Anaimba nyimbo zasopano pamaso pa Mulungu, zamoyo zinai na akulu. Kunalibe wina opunzira nyimbo imeneyi koma chabe aja 144,000 omwe anaguliwa pa dziko la pansi. Aba nibaja bamene sanazidese na akazi, cifukwa anazisunga ku chiwelewele. Niyaba amene alondola mwana wa nkhosa kulikonse kwamene ayenda. Awa anaguliwa kuchoka pa anthu ngati ana oyamba a Mulungu ni mwana wa nkhosa. Palibe boza yamene inapezeka mkamwa mwao; niopanda \v 3 \v 4 \v 5 Anaimba nyimbo zasopano pamaso pa Mulungu, zamoyo zinai na akulu. Kunalibe wina opunzira nyimbo imeneyi koma chabe aja 144,000 omwe anaguliwa pa dziko la pansi. Aba nibaja bamene sanazidese na akazi, cifukwa anazisunga ku chiwelewele. Niyaba amene alondola mwana wa nkhosa kulikonse kwamene ayenda. Awa anaguliwa kuchoka pa anthu ngati ana oyamba a Mulungu ni mwana wa nkhosa. Palibe boza yamene inapezeka mkamwa mwao; niopanda chifukwa.

1
14/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 \v 7 Ninaona mngelo wina akuuluka mu mwamba, amene anali na uthenga wa moyo ouza anthu onkhala pa ziko la pansi-