Wed Jan 23 2019 18:02:35 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
faf7b40cb7
commit
13ae30bb3d
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 3 \v 4 \v 5 Mngelo wina anabwera, ananyamula mbale ya golide ya zonunkhirisa, kuimilira pa guwa la zonunkhirisa. Zonunkhirisa zambiri zinapasidwa kwa iye kuti apereke pamozi na mapemphero ya okhulupilira pa guwa la zonunkhirisa pa mpando wa chimfumu. Utsi wa zonunkhirisa, na mapemphero ya okhulupirira, yanafikira ku mpando wa Mulungu kuchoka ku manja ya mngelo. Mngelo anatenga mbale ya zonunkhira na kuikamo moto wa pa guwa. Ndipo anaiponya pansi pa dziko la pansi, ndipo panali
|
||||
\v 3 \v 4 \v 5 Mngelo wina anabwera, ananyamula mbale ya golide ya zonunkhirisa, kuimilira pa guwa la zonunkhirisa. Zonunkhirisa zambiri zinapasidwa kwa iye kuti apereke pamozi na mapemphero ya okhulupilira pa guwa la zonunkhirisa pa mpando wa chimfumu. Utsi wa zonunkhirisa, na mapemphero ya okhulupirira, yanafikira ku mpando wa Mulungu kuchoka ku manja ya mngelo. Mngelo anatenga mbale ya zonunkhira na kuikamo moto wa pa guwa. Ndipo anaiponya pansi pa dziko la pansi, ndipo panali phokoso la kaleza, kugunda na kung'anipa kwa mphenzi, na chibvomezi.
|
Loading…
Reference in New Issue