nya-x-nyanja_rev_text_reg/16/08.txt

1 line
253 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 8 \v 9 Mngelo wa chinai anathira mbale yake ku zuba, ndipo inapasidwa chilolezo chotentha anthu na muliro. Anatenthedwa na kupya kwakukulu, ndipo ananyoza zina la Mulungu, amene ali na mphamvu pa ziwawa zimenezi. Sibanalape kapena kumupasa ulemelero.