nya-x-nyanja_rev_text_reg/06/15.txt

1 line
290 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 15 \v 16 \v 17 Ndipo mamfumu na anthu olemekezeka, akulu a asilikali, olemera, amphamvu, ena onse, omasuka ni akapolo, anabisala mu mphanga na mu minyala ya m'mapiri. Ananena kwa miyala na mapiri, "Tigweleni!" tibiseni ku nkhope ya iye amene ali pa mpando wa chimfumu ni kmwana wa nkhosa