nya-x-nyanja_rev_text_reg/21/16.txt

1 line
305 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 16 \v 17 mzinda unali olingana mbali zonse; utali wake unali olingana na ukula kwake. anapima mzinda na kopimila, 12000 kutalika kwake (kutalika, m'mimba ni kukula kwake kunali chimozi-mozi). anapimaso mpanda wake 144 cubits unenepa kwake kulingana na kupima kwa munthu (komwe ni kupimanso kwa mngelo).