Thu Jan 02 2020 18:57:53 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
a5e9b86d43
commit
f7f63c508c
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 12
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 3 \v 4 \v 5 Anaimba nyimbo zasopano pamaso pa Mulungu, zamoyo zinai na akulu. Kunalibe wina opunzira nyimbo imeneyi koma chabe aja 144,000 omwe anaguliwa pa dziko la pansi. Aba nibaja bamene sanazidese na akazi, cifukwa anazisunga ku chiwelewele. Niyaba amene alondola mwana wa nkhosa kulikonse kwamene ayenda. Awa anaguliwa kuchoka pa anthu ngati ana oyamba a Mulungu ni mwana wa nkhosa. Palibe boza yamene inapezeka mkamwa mwao; niopanda chifukwa.
|
||||
\v 3 Anaimba nyimbo zasopano pamaso pa Mulungu, zamoyo zinai na akulu. Kunalibe wina opunzira nyimbo imeneyi koma chabe aja 144,000 omwe anaguliwa pa dziko la pansi. \v 4 Aba nibaja bamene sanazidese na akazi, cifukwa anazisunga ku chiwelewele. Niyaba amene alondola mwana wa nkhosa kulikonse kwamene ayenda. Awa anaguliwa kuchoka pa anthu ngati ana oyamba a Mulungu ni mwana wa nkhosa. \v 5 Palibe boza yamene inapezeka mkamwa mwao; niopanda chifukwa.
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 6 \v 7 Ninaona mngelo wina akuuluka mu mwamba, amene anali na uthenga wa moyo ouza anthu onkhala pa ziko la pansi-ku maiko onse, mitundu yonse, chilankhulo na anthu. Anaitana na mau a mphamvu, "yopani Mulungu na kumupasa ulemelero. Chifukwa nthawi ya chiweruzo chake chafika. Mulambileni, wamene anapanga kumwamba, dziko la pansi, nyanja, na nyenje za manzi."
|
||||
\v 6 Ninaona mngelo wina akuuluka mu mwamba, amene anali na uthenga wa moyo ouza anthu onkhala pa ziko la pansi-ku maiko onse, mitundu yonse, chilankhulo na anthu. \v 7 Anaitana na mau a mphamvu, "yopani Mulungu na kumupasa ulemelero. Chifukwa nthawi ya chiweruzo chake chafika. Mulambileni, wamene anapanga kumwamba, dziko la pansi, nyanja, na nyenje za manzi."
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 9 \v 10 Mngelo wina-mngelo wachitatu- anawalondola kukamba ati na mau okuwa, "ngati wina apembeza chilombo na chifano chake, na kupasiwa namba pa mphumi kapena pa zanja lake, azamwa vinyo wa mkwiyo wa Mulungu, vinyo wamene waikiwa opanda kutirako manzi mu cup ya kukalipa kwake. Munthu amene azamwa azabvutika na muliro na sufule pamenso pa angelo na mwana wa nkhosa."
|
||||
\v 9 Mngelo wina-mngelo wachitatu- anawalondola kukamba ati na mau okuwa, "ngati wina apembeza chilombo na chifano chake, na kupasiwa namba pa mphumi kapena pa zanja lake, \v 10 azamwa vinyo wa mkwiyo wa Mulungu, vinyo wamene waikiwa opanda kutirako manzi mu cup ya kukalipa kwake. Munthu amene azamwa azabvutika na muliro na sufule pamenso pa angelo na mwana wa nkhosa."
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 11 \v 12 Utsi wa kunzunzika kwao upitilira ku mwamba nthawi zonse, ndipo sapumula usana na usiku-awa opembeza chilombo na fano lake, na aliyese amene analandira chizindikiro cha zina lake. Apa pali kufunika kupilira kwa iwo amene ni oyera, amene akonkha malamulo ya Mulungu na chikhulupiliro mwa Yesu."
|
||||
\v 11 Utsi wa kunzunzika kwao upitilira ku mwamba nthawi zonse, ndipo sapumula usana na usiku-awa opembeza chilombo na fano lake, na aliyese amene analandira chizindikiro cha zina lake. \v 12 Apa pali kufunika kupilira kwa iwo amene ni oyera, amene akonkha malamulo ya Mulungu na chikhulupiliro mwa Yesu."
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 14 \v 15 \v 16 Ninayangana, ndipo panali makumbi yoyera. Ndipo onkhala pa makumbi anali ngati mwana wa munthu. Anali na kolona ya golide pa mutu pake na chikwakwa chonola ku manja yake. Ndipo mngelo wina anatuluka mu nyumba ya Mulungu ndipo anaitana na mau okweza kuitana uja amene ali pa makumbi: "Tenga chikwakwa chako elo uyambe kujuba. Chifukwa nthawi yojuba yakwana, cifukwa zokolola pa ziko zapya." Ndipo wamene anali pa makumbi anayamba kuyendesa chikwakwa pa ziko, ndipo ziko inakololedwa.
|
||||
\v 14 Ninayangana, ndipo panali makumbi yoyera. Ndipo onkhala pa makumbi anali ngati mwana wa munthu. Anali na kolona ya golide pa mutu pake na chikwakwa chonola ku manja yake. \v 15 Ndipo mngelo wina anatuluka mu nyumba ya Mulungu ndipo anaitana na mau okweza kuitana uja amene ali pa makumbi: "Tenga chikwakwa chako elo uyambe kujuba. Chifukwa nthawi yojuba yakwana, cifukwa zokolola pa ziko zapya." \v 16 Ndipo wamene anali pa makumbi anayamba kuyendesa chikwakwa pa ziko, ndipo ziko inakololedwa.
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 17 \v 18 Mngelo wina anatuluka ku mwamba mu nyumba ya Mulungu; nayeve anali na chikwakwa. Mngelo winanso anatuluka kuchoka pa guwa la zonunkhirisa, amene anali na ulamuliro pa muliro. Anaitana na mphamvu uja amene anali na chikwakwa chonola, "Tenga chikwakwa chako na kuika pamozi zidunswa za mpesa m'minda ya ziko, chifukwa mpesa wake wapya."
|
||||
\v 17 Mngelo wina anatuluka ku mwamba mu nyumba ya Mulungu; nayeve anali na chikwakwa. \v 18 Mngelo winanso anatuluka kuchoka pa guwa la zonunkhirisa, amene anali na ulamuliro pa muliro. Anaitana na mphamvu uja amene anali na chikwakwa chonola, "Tenga chikwakwa chako na kuika pamozi zidunswa za mpesa m'minda ya ziko, chifukwa mpesa wake wapya."
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 19 \v 20 Mngelo anayendesa chikwakwa chake pa ziko nakutenga zidunswa za mpesa. Anaiponya motwera mpesa wa mkwiyo wa Mulungu. Ndipo motwera mpesa munaponyewa panja pa mzinda, ndipo magazi anathiridwa kuchoka mwaicho kufika pakamwa pa akavalo, ma stadia 1,600.
|
||||
\v 19 Mngelo anayendesa chikwakwa chake pa ziko nakutenga zidunswa za mpesa. Anaiponya motwera mpesa wa mkwiyo wa Mulungu. \v 20 Ndipo motwera mpesa munaponyewa panja pa mzinda, ndipo magazi anathiridwa kuchoka mwaicho kufika pakamwa pa akavalo, ma stadia 1,600.
|
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 3 \v 4 Anali kuimba nyimbo ya Mose, kapolo wa Mulungu, nyimbo ya mwana wa nkhosa: "Nchito zanu ni zabwino komanso za mphamvu, ambuye Mulungu, wa mphamvu zonse. Njira zanu ni zabwino ni za chilungamo, mfumu ya maiko onse. Ndani wamene sazakuyopani, Ambuye, nakukweza zina lanu? Chifukwa inu nokha ndinu oyera. Maiko onse yazabwera kukupembezani cifukwa cha nchito zanu zoyera zomwe zavumbulusidwa."
|
||||
\v 3 Anali kuimba nyimbo ya Mose, kapolo wa Mulungu, nyimbo ya mwana wa nkhosa: "Nchito zanu ni zabwino komanso za mphamvu, ambuye Mulungu, wa mphamvu zonse. Njira zanu ni zabwino ni za chilungamo, mfumu ya maiko onse. \v 4 Ndani wamene sazakuyopani, Ambuye, nakukweza zina lanu? Chifukwa inu nokha ndinu oyera. Maiko onse yazabwera kukupembezani cifukwa cha nchito zanu zoyera zomwe zavumbulusidwa."
|
|
@ -140,6 +140,21 @@
|
|||
"11-16",
|
||||
"11-18",
|
||||
"11-19",
|
||||
"12-title",
|
||||
"14-title",
|
||||
"14-03",
|
||||
"14-06",
|
||||
"14-08",
|
||||
"14-09",
|
||||
"14-11",
|
||||
"14-13",
|
||||
"14-14",
|
||||
"14-17",
|
||||
"14-19",
|
||||
"15-title",
|
||||
"15-01",
|
||||
"15-02",
|
||||
"15-03",
|
||||
"17-title"
|
||||
]
|
||||
}
|
Loading…
Reference in New Issue