1 line
295 B
Plaintext
1 line
295 B
Plaintext
\v 18 Chisoni changa chilibe mapeto, ndipo mtima wanga ukudwala. \v 19 Taonani! Mawu ofuula a mwana wamkazi wa anthu anga ochokera kudziko lakutali! Kodi Yehova sali mu Ziyoni? Kodi mfumu yake kulibenso? Nanga bwanji akuutsa mkwiyo wanga ndi mafano ao osema, ndi mafano ao opanda pake achilendo? |