1 line
499 B
Plaintext
1 line
499 B
Plaintext
\v 10 \v 11 Chotero iwe, mtumiki wanga Yakobo, usaope, atero Yehova, ndipo usachite mantha, iwe Isiraeli. pakuti taona, ndidzakubweza iwe kucokera kutali, ndi ana ako ku dziko la ndende. Yakobo adzabwera, nadzakhala pamtendere; adzakhala wokhazikika, ndipo sipadzakhalanso choopsa. Pakuti ine ndili ndi iwe, watero Yehova, kuti ndikupulumutse. Kenako ndidzathetsa mitundu yonse ya anthu kumene ndinakubalalitsirani. Koma sindidzakuthawitsa, ngakhale ndikulanga koyenera, osadzakusiya wosakulangidwa. |