1 line
524 B
Plaintext
1 line
524 B
Plaintext
\v 14 Chotero iwe, Yeremiya, usapempherere anthu awa. Musawalire kapena kuwapempherera. Pakuti sindidzamvera pamene adzandiitana m’tsoka lawo. \v 15 Chifukwa chiyani wokondedwa wanga, amene wakhala ndi zolinga zoipa zambiri, ali m'nyumba mwanga? Nyama ya nsembe zanu sizingakuthandizeni. Mumasangalala chifukwa cha zochita zanu zoipa. \v 16 Kale Yehova anakutcha mtengo waazitona wamasamba, wokongola ndi zipatso zokoma; Koma adzayatsa moto umene udzamveka ngati mkokomo wa mphepo yamkuntho; nthambi zake zidzathyoledwa. |