2 lines
534 B
Plaintext
2 lines
534 B
Plaintext
\v 6 Yehova anati kwa ine, Lengeza zonsezi m'midzi ya Yuda ndi m'misewu ya Yerusalemu. Nena, Mverani mawu a pangano ili ndi kuwachita. \v 7 Pakuti ndakhala ndikulamulira makolo anu kuyambira tsiku lija ndinawatulutsa m’dziko la Aigupto kufikira lero lino, ndikuwachenjeza kosalekeza, ndi kuti, Mverani mawu anga.
|
||
\v 8 Koma sanamvere, kapena kutchera khutu. Aliyense wakhala akuyenda mu kuumitsa kwa mtima wake woipa. Choncho ndinabweretsa matemberero onse a m’pangano limene ndinawalamula kuti liwagwere. Koma anthu sanamverebe. |