1 line
278 B
Plaintext
1 line
278 B
Plaintext
|
\v 18 \v 19 Yehova wanena kuti: “Taonani, ndidzabweretsanso anthu amene anagwidwa a m’mahema a Yakobo ndipo ndidzachitira chifundo nyumba zake. nyimbo yotamanda ndi yosangalatsa idzatuluka mwa iwo, pakuti ndidzawachulukitsa, osawachepetsa, ndidzawalemekeza kuti asachepetse.
|