1 line
338 B
Plaintext
1 line
338 B
Plaintext
|
\v 9 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Chiwembu chapezeka mwa anthu a Yuda ndi okhala mu Yerusalemu. \v 10 Iwo atembenukira ku mphulupulu za makolo awo oyambirira, amene anakana kumvera mawu anga, amene anatsatira milungu ina ndi kuigwadira. Nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda inaphwanya pangano limene ndinapangana ndi makolo awo.
|