\v 11 yuda anati kuli Tama, muoungozi wake, "Upitise kunkhala wofesdwa munyumba yabatate bako kafika sela, mwana wanga, akakule."chifukwa anayopa, " Kuti angafe nayeve, monga abale bake." Tama ayenda kunkhala munyumba yabatate bake.