\c 5 \v 1 Iyi ndiye mbili ya bobadwa kwa Adamu pasiku lamene Mulungu anapanga mutundu wa anabapanga bolingana naye. \v 2 Mwamuna na mukazi anabapanga. Anabadalisa nakuba pasa zina kuti bantu pamene anabapanga.