nya-x-nyanja_gen_text_reg/45/01.txt

1 line
428 B
Plaintext

\c 45 \v 1 Ndipo Yosefe anakangiwa kuzilesa kuti asalile pa menso pa banchito bake. Anakamba mopunda, " Bonse banisiye," panalibe wanchito aliyense pamene Yosefe anaziulula kuli ba bale bake. \v 2 Analila na chongo, ndipo Aigupto bananvela, na nyumba ya Farao inanvela. \v 3 Yosefe anati kuli ba bale bake, " Ine ndine Yosefe. Ushe batate banga bakali moyo?" Koma ba bale bake sibanamuyake, chifukwa banali namata pamenso pake.