nya-x-nyanja_gen_text_reg/47/27.txt

1 line
229 B
Plaintext

\v 27 Ndipo Israeli anakhala mu Igipito, mu malo ya Gosheni. Batu bake bankhala ndi zintau kumene kuja. Bana paka kwabili. \v 28 Yakobo anakala mu Igipito zaka seventini, ndipo zaka za umoyo wa Yakobo zinali handredi foti seveni.