nya-x-nyanja_gen_text_reg/42/18.txt

1 line
350 B
Plaintext

\v 18 Yosefe anakamba nabeve pasiku yacitatu, " Citani ici kuti mukhale namoyo, Popeza niyopa Mulungu. \v 19 Ngati ndimwe bamuna bazo ona, lekani umozi wa abale wanu akhale mundende iyi, koma imwe mu yende, nyamulani vokodya vanjala ya manyumba yanu. \v 20 Bwelesani mufana wanu kuti mau yanu ya simikiziwe ndipo simuza mwalila." Ndio banacita zimezo