nya-x-nyanja_gen_text_reg/38/17.txt

1 line
329 B
Plaintext

\v 17 Mwamuna anakamba kuti, "Niza kutumila kambuzi kang'ono kuchoka kuzobeta." mukazi anakamba kuti, "uzampasa lowezo kufikila ukatume?" \v 18 Mwamuna anakamba kuti, "Nilonjezo bwanji yeningakupase? mukazi anayanka, "chidindo na ntambo yako na ndondo ili mumanja yako."Anamupasa no yenda kuli eve, ndipo anankhala na mimba yake.