1 line
363 B
Plaintext
1 line
363 B
Plaintext
\v 4 Yakobo anakamba kuli benve kuti, "ba bale banga, mwachokela kuti?' bana yanka, "Tachokela ku Haran." Anakamba kuli benve, \v 5 "Mumuziba Labani mwana mwamuna wa Naha? "Nabenve banakamba kuti, "Timuziba. " \v 6 anakamba kuli benve kuti, "mwati alibwino?" Benve banakamba kuti, " alichabe bwino, na, yangananei kuja, Recho mwana wake mukazi abwela na mbelele." |