|
\v 23 Pamene zuba inekwele pa ziko Loti anali anafika ku Zowa. \v 24 Yehova analokesa nvula ya Saufa mu mulilo kuchokela kumwamba mu sodom na Gomora. \v 25 Ana wononga mizinda zija, an malo yalibe kantu kalikoonse , nazonse zamoyo zinanili mumuzinda, nazonse zomela pansi. |