1 line
415 B
Plaintext
1 line
415 B
Plaintext
\v 18 Loti anati kuli Beeve, "iyaye, napapata, bakulu banchito yanga! \v 19 Wanchito wanu apeza chisomo pamenso yanu, anso mwanilangisa chifundo chopitilila mukupulumusa umoyo wanga. Ndipo siningtamangile kulupili, chifukwa chiwonongeko chachikulu chinganipeze, ndipo nizafa. \v 20 Wona, uja muzinda alipafupi maningi kutabilako, anso nikang'ono napapata, lekani niyenda (sikangono?), Ndipo umoyo wanga uzapulumuka. |