1 line
335 B
Plaintext
1 line
335 B
Plaintext
\v 6 Ndipo Loti ananyenda panja pachiseko no vala chiseko kumbuyo kwake. \v 7 Akamba, " Namimpempani abbale banga, musachite zo chimwa. \v 8 wayonani, nilina bana bakazi babili bekakalibe kuziba mwamuna. nivomeleseni, niku papatani, kuti nibalete kuli imwe, ndipo muzachita zo kondwelesa aba, chifukwa bamu chinvili chamutenge wanga." |