|
\v 15 Pamene Yuda anamuwona anaganiza monga nimukazi wachiwele wele chifukwa enze anabisa nkope yake. \v 16 Anyenda kuli eve ndipo anti, "Bwela, leka naiwe chifukwa sana zibe kuti nimupongozi wake mukazi ndipo mukazi anakamba kuti, "Uzani pasa chani ukagona naine?" |